Ezekieli 33:15 BL92

15 woipayo akabweza cikole, nakabweza ico anacilanda mwacifwamba, nakayenda m'malemba a moyo wosacita cosalungama, adzakhala ndi moyo ndithu, sadzafa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 33

Onani Ezekieli 33:15 nkhani