Ezekieli 33:20 BL92

20 Koma munati, Njira ya Ambuye siiyenera. Nyumba ya Israyeli inu, ndidzakuweruzani, yense monga mwa njira zace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 33

Onani Ezekieli 33:20 nkhani