Ezekieli 34:18 BL92

18 Kodi cikuceperani, kuti mwadya podyetsa pabwino? muyenera kodi kupondereza ndi mapazi anu podyera panu potsala? muyenera kumwa madzi ndikha, ndi kubvundulira otsalawo ndi mapazi anu?

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34

Onani Ezekieli 34:18 nkhani