23 Ndipo ndidzaziutsira mbusa mmodzi; iye adzazidyetsa, ndiye mtumiki wanga Davide, iye adzazidyetsa, nadzakhala mbusa wao.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34
Onani Ezekieli 34:23 nkhani