25 Ndipo ndidzapangana nazo pangano la mtendere, ndi kuleketsa zirombo zoipa m'dzikomo; ndipo zidzakhala mosatekeseka m'cipululu, ndi kugona kunkhalango.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34
Onani Ezekieli 34:25 nkhani