Ezekieli 34:4 BL92

4 Zofoka simunazilimbitsa; yodwala simunaiciritsa, yotyoka simunailukira chika, yopitikitsidwa simunaibweza, yotayika simunaifuna; koma munazilamulira mwamphamvu ndi moopsa,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34

Onani Ezekieli 34:4 nkhani