3 nuti nalo, Atero Ambuye Yehova, Taona, ndiipidwa nawe phiri la Seiri, ndipo ndidzakutambasulira dzanja langa, ndi kukusanduliza lacipululu ndi lodabwitsa.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 35
Onani Ezekieli 35:3 nkhani