6 cifukwa cace, Pali Ine, ati Ambuye Yehova, ndikukonzeratu uphedwe, ndi mwazi udzakulondola; popeza sunadana nao mwazi, mwazi udzakulondola.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 35
Onani Ezekieli 35:6 nkhani