21 Koma ndinawaleka cifukwa ca dzina langa loyera, limene a nyumba ya Israyeli adalidetsa pakati pa amitundu, kumene adarakako,
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36
Onani Ezekieli 36:21 nkhani