Ezekieli 36:24 BL92

24 Pakuti ndidzakutengani kukuturutsani kwa amitundu, ndi kukusokolotsani m'maiko onse, ndi kubwera nanu m'dziko lanu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36

Onani Ezekieli 36:24 nkhani