26 Ndipo ndidzakupatsani mtima watsopano, ndi kulonga m'kati mwanu mzimu watsopano; ndipo ndidzacotsa mtima wamwala m'thupi, ndi kukupatsani mtima wamnofu.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36
Onani Ezekieli 36:26 nkhani