Ezekieli 36:38 BL92

38 Ngati nkhosa za nsembe, ngati nkhosa za ku Yerusalemu pa madyerero ace oikika, momwemo midzi yamabwinja idzadzala nao magulu a anthu; motero adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36

Onani Ezekieli 36:38 nkhani