Ezekieli 37:11 BL92

11 Pamenepo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, Mafupa awa ndiwo nyumba yonse ya Israyeli; taonani, akuti, Mafupa athu auma, ciyembekezo cathu catayika, talikhidwa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 37

Onani Ezekieli 37:11 nkhani