Ezekieli 37:13 BL92

13 Ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine. Yehova potsegula Ine kumanda kwanu, ndi kukweza inu kukuturutsani m'manda mwanu, anthu anga inu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 37

Onani Ezekieli 37:13 nkhani