Ezekieli 37:3 BL92

3 Ndipo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, mafupa awa nkukhala ndi moyo kodi? Ndipo ndinati, Ambuye Yehova, mudziwa ndinu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 37

Onani Ezekieli 37:3 nkhani