Ezekieli 37:8 BL92

8 Ndipo ndinapenya, taonani, panali mitsempha pa iwo, panadzaponso mnofu, ndi khungu linawakuta pamwamba pace; koma munalibe mpweya mwa iwo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 37

Onani Ezekieli 37:8 nkhani