14 Cifukwa cace nenera, wobadwa ndi munthu iwe, uziti kwa Gogi, Atero Ambuye Yehova, Tsiku ilo, pokhala mosatekeseka anthu anga Israyeli, sudzacidziwa kodi?
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 38
Onani Ezekieli 38:14 nkhani