Ezekieli 38:9 BL92

9 Ndipo udzakwera udzadza ngati mkuntho, udzanga mtambo kuphimba dziko, iwe ndi magulu ako onse, ndi mitundu yambiri ya anthu pamodzi ndi iwe.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 38

Onani Ezekieli 38:9 nkhani