Ezekieli 39:1 BL92

1 Ndipo iwe, wobadwa ndi munthu, nenera motsutsana naye Gogi, uziti, Atero Ambuye Yehova, Taona, nditsutsana nawe Gogi, iwe mfumu yaikuru ya Meseki ndi Tubala;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 39

Onani Ezekieli 39:1 nkhani