Ezekieli 39:15 BL92

15 Ndipo opitapitawo adzapitapita m'dziko, ndipo winaakaona pfupa la munthu aikepo cizindikilo, mpaka oikawo aliika m'cigwa ca unyinji wa Gogi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 39

Onani Ezekieli 39:15 nkhani