Ezekieli 40:17 BL92

17 Pamenepo analowa nane ku bwalo lakunja, ndipo taonani, panali zipinda, ndi moyalidwa miyala mokonzekera bwalo pozungulira ponse; moyalidwa miyalamo munali zipinda makumi atatu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:17 nkhani