27 Ndipo panali cipata ca bwalo lam'kati cakulozakumwela, nayesa kuyambira kucipata kufikira kucipata kumwela mikono zana.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40
Onani Ezekieli 40:27 nkhani