Ezekieli 40:3 BL92

3 Ndipo anamuka nane komweko, ndipo taona, panali munthu, maonekedwe ace ngati amkuwa, ndi cingwe cabwazi m'dzanja lace, ndi bango loyesa nalo, naima kucipata iye.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:3 nkhani