Ezekieli 40:43 BL92

43 Ndi ziciri zangowe, cikhato m'litali mwace, zinamangika m'katimo pozungulirapo; ndi pamagome panali nyama ya nsembe.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:43 nkhani