Ezekieli 40:47 BL92

47 Ndipo anayesa bwalolo mikono zana m'litali mwace, ndi mikono zana kupingasa kwace, lamphwamphwa; ndi guwa la nsembe linali kukhomo kwa nyumba.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:47 nkhani