Ezekieli 41:1 BL92

1 Ndipo anadza nane ku Kacisi, nayesa nsanamira zace, kupingasa kwace mikono isanu ndi umodzi cakuno, ndi mikono isanu ndi umodzi cauko, ndiko kupingasa kwa cihema cija.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 41

Onani Ezekieli 41:1 nkhani