Ezekieli 41:11 BL92

11 Ndi makomo a zipinda za m'mphepete analoza kumpatawo, khomo lina kumpoto, ndi lina kumwela; ndi malo a pa mpatawo anayesa mikono isanu kupingasa kwace pozungulira pace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 41

Onani Ezekieli 41:11 nkhani