Ezekieli 41:17 BL92

17 kufikira pamwamba pa khomo, mpaka nyumba ya m'katimo, ndi kunja kwace, ndi khoma lonse kwete m'kati ndi kunja, monga mwa miyeso.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 41

Onani Ezekieli 41:17 nkhani