Ezekieli 41:22 BL92

22 Guwa la nsembe linali lamtengo, msinkhu wace mikono itatu, ndi m'litali mwace mikono iwiri, ndi ngondya zace, ndi tsinde lace, ndi: thupi, nza mtengo; ndipo ananena ndi ine, Ili ndiko gome liri pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 41

Onani Ezekieli 41:22 nkhani