Ezekieli 41:24 BL92

24 Ndipo pamakomopo panali zitseko zopatukana zotembenuzika, cina copatukana pa khomo lina cina pa linzace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 41

Onani Ezekieli 41:24 nkhani