Ezekieli 41:8 BL92

8 Ndinaonanso kuti kunyumba kunali ciunda pozungulira pace; maziko a zipinda za m'mphepete anafikira muyeso wa bango la mikono isanu ndi umodzi yaikuru.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 41

Onani Ezekieli 41:8 nkhani