Ezekieli 42:16 BL92

16 Anayesa mbali ya kum'mawa ndi bango loyesera, mabango mazana asanu, kuyesa ndi bango loyesera, pozungulira pace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 42

Onani Ezekieli 42:16 nkhani