3 Pandunji pa mikono makumi awiri a bwalo lam'kati, ndi pandunji pa moyalamo mwa miyala, mwa bwalo lakunja, panali khonde lam'mwamba, lokomana ndi khonde linzace losanjikika paciwiri.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 42
Onani Ezekieli 42:3 nkhani