10 Wabadwa ndi munthu iwe, onetsa nyumba ya Israyeli kacisiyu, kuti acite manyazi ndi mphulupulu zao; ndipo ayese muyeso wace.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43
Onani Ezekieli 43:10 nkhani