12 Lamulo la kacisi ndi ili: pamwamba pa phiri malire ace onse pozungulira pace azikhala opatulikitsa. Taonani, limeneli ndi lamulo la kacisi.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43
Onani Ezekieli 43:12 nkhani