Ezekieli 43:16 BL92

16 Ndi pamoto pa guwa, m'litali mwace mikono khumi ndi iwiri, ndi kupingasa kwace khumi ndi iwiri, lampwamphwa mbali zace zinai.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43

Onani Ezekieli 43:16 nkhani