Ezekieli 43:25 BL92

25 Masiku asanu ndi awiri uzikonzera mbuzi tsiku ndi tsiku, ikhale nsembe yaucimo; akonzerenso mwana wa ng'ombe, ndi nkhosa yamphongo ya zoweta zopanda cirema.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43

Onani Ezekieli 43:25 nkhani