Ezekieli 43:5 BL92

5 Ndipo mzimu unandinyamula numuka nane ku bwalo la m'kati; ndipo taonani, ulemerero wa Mulungu unadzaza kacisi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43

Onani Ezekieli 43:5 nkhani