11 Efa ndi bati zikhale za muyeso umodzi, bati liyese limodzi la magawo khumi la homeri, efa lomwe liyese limodzi la magawo khumi la homeri; muyeso wao uyesedwa monga mwa homeri.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45
Onani Ezekieli 45:11 nkhani