Ezekieli 45:19 BL92

19 Ndipo wansembe atengeko mwazi wa nsembe yaucimo, naupake pa mphuthu za kacisi, ndi pa ngondya zinai za phaka la guwa la nsembe, ndi pa mphuthu za cipata ca bwalo lam'kati.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45

Onani Ezekieli 45:19 nkhani