22 Ndipo tsiku lomwelo kalonga adzikonzere yekha ndi anthu onse a m'dziko ng'ombe, ikhale ya nsembe yaucimo.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45
Onani Ezekieli 45:22 nkhani