8 M'dzikomo ili lidzakhala lace lace m'Israyeli; ndipo akalonga anga sadzazunzanso anthu anga, koma adzapereka dziko kwa nyumba ya Israyeli monga mwa mapfuko ao.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45
Onani Ezekieli 45:8 nkhani