13 Uziperekanso kwa Yehova mwana wa nkhosa wa caka cimodzi akhale nsembe yopsereza wopanda cirema, tsiku ndi tsiku, m'mawa ndi m'mawa, uzimpereka.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 46
Onani Ezekieli 46:13 nkhani