Ezekieli 46:24 BL92

24 Ndipo anati kwa ine, Izi ndi nyumba zophikiramo, kumene atumiki a kacisi aziphikira nsembe ya anthu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 46

Onani Ezekieli 46:24 nkhani