3 Poturuka munthuyu kumka kum'mawa ndi cingwe coyesera m'dzanja lace, anayesa mikono cikwi cimodzi, nandipititsa pamadzi, madzi oyesa m'kakolo.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 47
Onani Ezekieli 47:3 nkhani