Ezekieli 48:11 BL92

11 Cidzakhala ca ansembe opatulidwa a ana a Zadoki, amene anasunga udikiro wanga osasokera, muja anasokera ana a Israyeli, ndi muja anasokera Alevi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 48

Onani Ezekieli 48:11 nkhani