Ezekieli 48:15 BL92

15 Ndipo zikwi zisanu zotsalazo m'kupingasa kwace, cakuno ca zikwi makumi awiri mphambu zisanu, zikhale za nchito wamba za mudzi, za kumangapo zapabusa; ndi mudzi ukhale pakati pace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 48

Onani Ezekieli 48:15 nkhani