22 Kuyambira tsono dziko la Alevi kufikira dziko la mudzi, ndiwo a pakati pa magawo ace a kalonga, pakati pa malire a Yuda ndi malire a Benjamini, kukhale kwa kalonga.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 48
Onani Ezekieli 48:22 nkhani