31 ndi zipata za mudzi zidzakhala monga mwa maina a mafuko a Israyeli; zipata zitatu kumpoto: cipata cimodzi ca Rubeni, cipata cimodzi ca Yuda, cipata cimodzi ca Levi;
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 48
Onani Ezekieli 48:31 nkhani