Ezekieli 48:35 BL92

35 Pozungulira pace ndipo mabango zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu, ndi dzina la mudziwo kuyambira tsiku ilo lidzakhala, Yehova ali pomwepo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 48

Onani Ezekieli 48:35 nkhani